Ndipo palibe cholengedwa chimene chimabisika pamaso pake

Ndipo palibe cholengedwa chimene chimabisika pamaso pake, koma zonse zikhala pambalambanda ndi poyera pamaso pake pa Iye amene tichita.

Ahebri 4:13